8 Ndikauza munthu woipa kuti, ‘Munthu woipa iwe, udzafa ndithu,’+ koma iwe osanena chilichonse pochenjeza woipayo kuti asinthe zochita zake, iyeyo adzafa monga munthu woipa chifukwa cha zolakwa zake,+ koma iwe ndidzakuimba mlandu chifukwa cha magazi ake.