Ezekieli 33:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma iwe ukachenjeza munthu woipa kuti asiye zinthu zoipa zimene akuchita, iye nʼkukana kusiya zoipazo, munthuyo adzafa chifukwa cha zolakwa zake,+ koma iweyo udzapulumutsa moyo wako ndithu.+
9 Koma iwe ukachenjeza munthu woipa kuti asiye zinthu zoipa zimene akuchita, iye nʼkukana kusiya zoipazo, munthuyo adzafa chifukwa cha zolakwa zake,+ koma iweyo udzapulumutsa moyo wako ndithu.+