Ezekieli 33:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiye iwe mwana wa munthu, uza nyumba ya Isiraeli kuti, ‘Inu mwanena kuti: “Kupanduka kwathu komanso machimo athu zikutilemera kwambiri, nʼkutichititsa kuti titope kwambiri.+ Ndiye tingapitirize bwanji kukhala ndi moyo?”’+
10 Ndiye iwe mwana wa munthu, uza nyumba ya Isiraeli kuti, ‘Inu mwanena kuti: “Kupanduka kwathu komanso machimo athu zikutilemera kwambiri, nʼkutichititsa kuti titope kwambiri.+ Ndiye tingapitirize bwanji kukhala ndi moyo?”’+