15 komanso munthu woipayo akabweza chinthu chimene anatenga kwa munthu amene anakongola zinthu zake,+ akabweza zinthu zimene analanda mwauchifwamba,+ nʼkuyamba kuyenda motsatira malamulo opatsa moyo popewa kuchita zinthu zoipa, ndithu munthuyo adzapitiriza kukhala ndi moyo.+ Iye sadzafa.