Ezekieli 33:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Sadzapatsidwa chilango chifukwa cha machimo amene anachitawo.+ Adzapitiriza kukhala ndi moyo chifukwa chochita zinthu motsatira malamulo ndiponso mwachilungamo.’+
16 Sadzapatsidwa chilango chifukwa cha machimo amene anachitawo.+ Adzapitiriza kukhala ndi moyo chifukwa chochita zinthu motsatira malamulo ndiponso mwachilungamo.’+