-
Ezekieli 33:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Koma anthu a mtundu wako anena kuti, ‘Njira za Yehova nʼzopanda chilungamo,’ pamene njira zawo ndi zimene zili zopanda chilungamo.
-