Ezekieli 33:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma inu mwanena kuti, ‘Njira za Yehova nʼzopanda chilungamo.’+ Inu a nyumba ya Isiraeli, ine ndidzaweruza aliyense wa inu mogwirizana ndi zochita zake.”
20 Koma inu mwanena kuti, ‘Njira za Yehova nʼzopanda chilungamo.’+ Inu a nyumba ya Isiraeli, ine ndidzaweruza aliyense wa inu mogwirizana ndi zochita zake.”