Ezekieli 33:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndiyeno madzulo, munthu amene anathawa uja asanafike, dzanja la Yehova linandikhudza ndipo Mulungu anatsegula pakamwa panga munthu uja asanafike mʼmawa. Choncho pakamwa panga panatseguka ndipo ndinayambanso kulankhula.+
22 Ndiyeno madzulo, munthu amene anathawa uja asanafike, dzanja la Yehova linandikhudza ndipo Mulungu anatsegula pakamwa panga munthu uja asanafike mʼmawa. Choncho pakamwa panga panatseguka ndipo ndinayambanso kulankhula.+