Ezekieli 33:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Choncho auze kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Inu mukudya nyama limodzi ndi magazi ake,+ mumadalira* mafano anu onyansa* ndipo mukupitiriza kukhetsa magazi.+ Ndiye pamenepa ndinu oyenera kutenga dzikoli kuti likhale lanu?
25 Choncho auze kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Inu mukudya nyama limodzi ndi magazi ake,+ mumadalira* mafano anu onyansa* ndipo mukupitiriza kukhetsa magazi.+ Ndiye pamenepa ndinu oyenera kutenga dzikoli kuti likhale lanu?