Ezekieli 33:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndidzachititsa kuti dzikolo likhale bwinja lowonongeka kwambiri.+ Ndidzathetsa kudzikuza komanso kunyada kwake ndipo mapiri a mu Isiraeli adzawonongedwa+ moti sipadzapezeka wodutsamo.
28 Ndidzachititsa kuti dzikolo likhale bwinja lowonongeka kwambiri.+ Ndidzathetsa kudzikuza komanso kunyada kwake ndipo mapiri a mu Isiraeli adzawonongedwa+ moti sipadzapezeka wodutsamo.