Ezekieli 33:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndikadzachititsa kuti dzikolo likhale bwinja lowonongeka kwambiri+ chifukwa cha zinthu zonse zonyansa zimene achita, iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.”’+
29 Ndikadzachititsa kuti dzikolo likhale bwinja lowonongeka kwambiri+ chifukwa cha zinthu zonse zonyansa zimene achita, iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.”’+