Ezekieli 33:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Iwo adzasonkhana nʼkukhala pamaso pako ngati anthu anga. Adzamva mawu ako koma sadzawatsatira.+ Chifukwa ndi pakamwa pawo, amakuuza zongofuna kukusangalatsa,* koma mtima wawo ukungofuna kupeza phindu mwachinyengo.
31 Iwo adzasonkhana nʼkukhala pamaso pako ngati anthu anga. Adzamva mawu ako koma sadzawatsatira.+ Chifukwa ndi pakamwa pawo, amakuuza zongofuna kukusangalatsa,* koma mtima wawo ukungofuna kupeza phindu mwachinyengo.