Ezekieli 34:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inu mukudya mafuta, ndipo mukuvala zovala zaubweya wa nkhosa. Mukupha nyama zonenepa kwambiri,+ koma nkhosa simukuzidyetsa.+
3 Inu mukudya mafuta, ndipo mukuvala zovala zaubweya wa nkhosa. Mukupha nyama zonenepa kwambiri,+ koma nkhosa simukuzidyetsa.+