Ezekieli 34:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Nkhosa zofooka simunazilimbitse ndipo zodwala simunazichiritse. Zovulala simunazimange. Nkhosa zosochera simunazibweze ndipo zimene zasowa simunazifufuze.+ Koma munkazilamulira mwankhanza komanso mopondereza.+
4 Nkhosa zofooka simunazilimbitse ndipo zodwala simunazichiritse. Zovulala simunazimange. Nkhosa zosochera simunazibweze ndipo zimene zasowa simunazifufuze.+ Koma munkazilamulira mwankhanza komanso mopondereza.+