10 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Ine nditsutsa abusawo ndipo ndiwauza kuti andibwezere nkhosa zanga. Ndiwaletsa kuti asamadyetse nkhosa zanga+ ndipo abusawo sadzadzidyetsanso okha. Ndidzalanditsa nkhosa zanga mʼkamwa mwawo ndipo sizidzakhalanso chakudya chawo.’”