Ezekieli 34:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndidzasamalira nkhosa zanga ngati mʼbusa amene wapeza nkhosa zake zimene zinabalalika ndipo akuzidyetsa.+ Ndidzazipulumutsa mʼmalo onse amene zinabalalikira pa tsiku la mitambo ndi mdima wandiweyani.+
12 Ndidzasamalira nkhosa zanga ngati mʼbusa amene wapeza nkhosa zake zimene zinabalalika ndipo akuzidyetsa.+ Ndidzazipulumutsa mʼmalo onse amene zinabalalikira pa tsiku la mitambo ndi mdima wandiweyani.+