Ezekieli 34:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ponena za inu nkhosa zanga, Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ine ndatsala pangʼono kuweruza pakati pa nkhosa ndi nkhosa inzake komanso pakati pa nkhosa zamphongo ndi mbuzi zamphongo.+
17 Ponena za inu nkhosa zanga, Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ine ndatsala pangʼono kuweruza pakati pa nkhosa ndi nkhosa inzake komanso pakati pa nkhosa zamphongo ndi mbuzi zamphongo.+