-
Ezekieli 34:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wauza nkhosazo kuti: “Ine ndilipo ndipo ndidzapereka chiweruzo pakati pa nkhosa yonenepa ndi nkhosa yowonda.
-