Ezekieli 34:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 ‘Zikadzatero, iwo adzadziwa kuti ine, Yehova Mulungu wawo, ndili nawo limodzi ndiponso kuti iwowo, a nyumba ya Isiraeli ndi anthu anga,’+ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”’
30 ‘Zikadzatero, iwo adzadziwa kuti ine, Yehova Mulungu wawo, ndili nawo limodzi ndiponso kuti iwowo, a nyumba ya Isiraeli ndi anthu anga,’+ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”’