Ezekieli 35:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chifukwa unanena kuti, ‘Mitundu iwiri iyi ya anthu ndi mayiko awiri awa zidzakhala zanga ndipo ife tidzatenga zonsezi.’+ Unanena zimenezi ngakhale kuti Yehova anali komweko. Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 35:10 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, tsa. 24
10 Chifukwa unanena kuti, ‘Mitundu iwiri iyi ya anthu ndi mayiko awiri awa zidzakhala zanga ndipo ife tidzatenga zonsezi.’+ Unanena zimenezi ngakhale kuti Yehova anali komweko.