Ezekieli 36:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndidzakupatsani mtima watsopano+ ndipo ndidzaika mzimu watsopano mwa inu.+ Ndidzachotsa mtima wamwala+ mʼmatupi anu nʼkukupatsani mtima wamnofu.* Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 36:26 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, tsa. 24
26 Ndidzakupatsani mtima watsopano+ ndipo ndidzaika mzimu watsopano mwa inu.+ Ndidzachotsa mtima wamwala+ mʼmatupi anu nʼkukupatsani mtima wamnofu.*