Ezekieli 37:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno anandifunsa kuti: “Iwe mwana wa munthu, kodi mafupawa angakhale ndi moyo?” Ine ndinayankha kuti: “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, inu ndi amene mukudziwa zimenezo.”+
3 Ndiyeno anandifunsa kuti: “Iwe mwana wa munthu, kodi mafupawa angakhale ndi moyo?” Ine ndinayankha kuti: “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, inu ndi amene mukudziwa zimenezo.”+