Ezekieli 37:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako anandiuza kuti: “Iwe mwana wa munthu, mafupawa akuimira nyumba yonse ya Isiraeli.+ Iwo akunena kuti, ‘Mafupa athu auma ndipo tilibenso chiyembekezo chilichonse.+ Tatheratu!’ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 37:11 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),3/2016, ptsa. 29-30 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, ptsa. 24-25
11 Kenako anandiuza kuti: “Iwe mwana wa munthu, mafupawa akuimira nyumba yonse ya Isiraeli.+ Iwo akunena kuti, ‘Mafupa athu auma ndipo tilibenso chiyembekezo chilichonse.+ Tatheratu!’