Ezekieli 37:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho losera, uwauze kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ine ndidzatsegula manda anu,+ inu anthu anga ndipo ndidzakutulutsani mʼmandamo nʼkukubweretsani mʼdziko la Isiraeli.+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 37:12 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, ptsa. 24-25
12 Choncho losera, uwauze kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ine ndidzatsegula manda anu,+ inu anthu anga ndipo ndidzakutulutsani mʼmandamo nʼkukubweretsani mʼdziko la Isiraeli.+