Ezekieli 37:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Anthu a mtundu wako* akakufunsa kuti, ‘Kodi sutiuza kuti zinthu zimenezi zikutanthauza chiyani?’