Ezekieli 37:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndidzachita nawo pangano lamtendere+ ndipo pangano limeneli lidzakhalapo mpaka kalekale. Ine ndidzachititsa kuti akhazikike mʼdzikolo ndipo ndidzawachulukitsa+ komanso ndidzaika malo anga opatulika pakati pawo mpaka kalekale. Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 37:26 Nsanja ya Olonda,3/15/2010, ptsa. 27-283/1/1991, ptsa. 18-19
26 Ndidzachita nawo pangano lamtendere+ ndipo pangano limeneli lidzakhalapo mpaka kalekale. Ine ndidzachititsa kuti akhazikike mʼdzikolo ndipo ndidzawachulukitsa+ komanso ndidzaika malo anga opatulika pakati pawo mpaka kalekale.