Ezekieli 38:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Khala wokonzeka, konzekera kumenya nkhondo, iweyo limodzi ndi asilikali ako onse amene asonkhana ndi iwe. Iweyo ukhala mtsogoleri* wawo.
7 Khala wokonzeka, konzekera kumenya nkhondo, iweyo limodzi ndi asilikali ako onse amene asonkhana ndi iwe. Iweyo ukhala mtsogoleri* wawo.