-
Ezekieli 38:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Udzapita kumeneko kuti ukalande komanso kutengako zinthu zambiri, ndiponso kuti ukaukire malo owonongedwa amene tsopano mukukhala anthu.+ Udzapita kukaukira anthu amene anasonkhanitsidwanso pamodzi kuchokera kumitundu ina,+ amene akusonkhanitsa chuma ndi katundu,+ komanso amene akukhala pakatikati pa dziko lapansi.
-