Ezekieli 38:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho losera, iwe mwana wa munthu, ndipo uuze Gogi kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Pa tsiku limenelo, anthu anga Aisiraeli akamadzakhala mwabata, ndithu iwe udzadziwa zimenezo.+
14 Choncho losera, iwe mwana wa munthu, ndipo uuze Gogi kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Pa tsiku limenelo, anthu anga Aisiraeli akamadzakhala mwabata, ndithu iwe udzadziwa zimenezo.+