Ezekieli 38:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Udzabwera kuchokera kumalo ako, kumadera akutali kwambiri akumpoto.+ Udzabwera ndi mitundu yambiri ya anthu. Anthuwo adzakhala gulu lalikulu, adzakhala chigulu chachikulu cha asilikali. Onsewo adzabwera atakwera pamahatchi.+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 38:15 Nsanja ya Olonda,7/1/1987, ptsa. 15-16
15 Udzabwera kuchokera kumalo ako, kumadera akutali kwambiri akumpoto.+ Udzabwera ndi mitundu yambiri ya anthu. Anthuwo adzakhala gulu lalikulu, adzakhala chigulu chachikulu cha asilikali. Onsewo adzabwera atakwera pamahatchi.+