Ezekieli 38:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 ‘Pa tsiku limenelo, tsiku limene Gogi adzalowe mʼdziko la Isiraeli, ndidzakhala ndi mkwiyo waukulu,’+ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa. Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 38:18 Ufumu wa Mulungu Ukulamulira, tsa. 227
18 ‘Pa tsiku limenelo, tsiku limene Gogi adzalowe mʼdziko la Isiraeli, ndidzakhala ndi mkwiyo waukulu,’+ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.