-
Ezekieli 38:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 ‘Ine ndidzalankhula mwaukali wanga woyaka moto komanso nditakwiya kwambiri. Ndipo pa tsiku limenelo mʼdziko la Isiraeli mudzachitika chivomerezi chachikulu.
-