Ezekieli 39:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iwe udzafera mʼmapiri a ku Isiraeli+ limodzi ndi magulu ako onse a asilikali ndi anthu a mitundu ina amene adzakhale nawe. Ndidzakuperekani kwa mbalame zamitundumitundu zodya nyama ndi zilombo zakutchire kuti mukhale chakudya chawo.”’+
4 Iwe udzafera mʼmapiri a ku Isiraeli+ limodzi ndi magulu ako onse a asilikali ndi anthu a mitundu ina amene adzakhale nawe. Ndidzakuperekani kwa mbalame zamitundumitundu zodya nyama ndi zilombo zakutchire kuti mukhale chakudya chawo.”’+