Ezekieli 39:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndidzachititsa kuti dzina langa loyera lidziwike pakati pa anthu anga Aisiraeli. Sindidzalolanso kuti dzina langa loyera lidetsedwe, ndipo anthu a mitundu ina adzadziwa kuti ine ndine Yehova,+ Mulungu Woyera mu Isiraeli.’+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 39:7 Nsanja ya Olonda,9/1/2012, tsa. 21
7 Ndidzachititsa kuti dzina langa loyera lidziwike pakati pa anthu anga Aisiraeli. Sindidzalolanso kuti dzina langa loyera lidetsedwe, ndipo anthu a mitundu ina adzadziwa kuti ine ndine Yehova,+ Mulungu Woyera mu Isiraeli.’+