Ezekieli 39:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 A nyumba ya Isiraeli adzatenga miyezi 7 akuika mʼmanda Gogi ndi gulu lake kuti ayeretse dzikolo.+