Ezekieli 39:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Ndidzabwezeretsa ana a Yakobo+ omwe anatengedwa kupita kumayiko ena ndipo ndidzachitira chifundo nyumba yonse ya Isiraeli.+ Ndi mphamvu zanga zonse, ndidzateteza dzina langa loyera.*+
25 Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Ndidzabwezeretsa ana a Yakobo+ omwe anatengedwa kupita kumayiko ena ndipo ndidzachitira chifundo nyumba yonse ya Isiraeli.+ Ndi mphamvu zanga zonse, ndidzateteza dzina langa loyera.*+