Ezekieli 39:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ndikadzawabweretsa kuchokera kumitundu ina ya anthu ndi kuwasonkhanitsa pamodzi kuchokera kumayiko a adani awo,+ ndidzadziyeretsa pakati pawo pamaso pa mitundu yambiri ya anthu.’+
27 Ndikadzawabweretsa kuchokera kumitundu ina ya anthu ndi kuwasonkhanitsa pamodzi kuchokera kumayiko a adani awo,+ ndidzadziyeretsa pakati pawo pamaso pa mitundu yambiri ya anthu.’+