Ezekieli 39:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 ‘Iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova Mulungu wawo, ndikadzawapititsa ku ukapolo pakati pa anthu a mitundu ina, kenako nʼkuwabwezeretsa kudziko lawo osasiyako wina aliyense.+
28 ‘Iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova Mulungu wawo, ndikadzawapititsa ku ukapolo pakati pa anthu a mitundu ina, kenako nʼkuwabwezeretsa kudziko lawo osasiyako wina aliyense.+