Ezekieli 39:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Sindidzawabisiranso nkhope yanga+ chifukwa panyumba ya Isiraeli ndidzatsanulirapo mzimu wanga,’+ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”
29 Sindidzawabisiranso nkhope yanga+ chifukwa panyumba ya Isiraeli ndidzatsanulirapo mzimu wanga,’+ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”