-
Ezekieli 40:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Kuchokera kutsogolo kwa khomo lakunja la kanyumba kapageti, kukafika kutsogolo kwa khonde, kumbali imene yayangʼanizana ndi kachisi, panali mikono 50.
-