-
Ezekieli 40:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Bwalo lamkati linali ndi geti limene linayangʼana kumʼmwera. Iye anayeza kuchokera pagetipo kulowera kumʼmwera kukafika pageti lina ndipo anapeza kuti panali mtunda wokwana mikono 100.
-