-
Ezekieli 40:40Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
40 Panja pa khomo lolowera mʼkanyumba kambali ya kumpoto panali matebulo awiri. Kumbali ina ya khonde la kanyumbako, kunalinso matebulo ena awiri.
-