-
Ezekieli 40:43Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
43 Kuzungulira khoma lonse lamkati anaikamo mashelefu amene anali chikhatho chimodzi mulifupi. Nyama za nsembe zimene ankapereka ngati mphatso ankaziika pamatebulo aja.
-