Ezekieli 41:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Kenako munthu uja anandipititsa mʼmalo oyera,* ndipo anayeza zipilala zamʼmbali. Chipilala cha mbali imodzi chinali mikono* 6 mulifupi ndipo cha mbali ina chinalinso mikono 6 mulifupi.
41 Kenako munthu uja anandipititsa mʼmalo oyera,* ndipo anayeza zipilala zamʼmbali. Chipilala cha mbali imodzi chinali mikono* 6 mulifupi ndipo cha mbali ina chinalinso mikono 6 mulifupi.