Ezekieli 41:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako analowa mʼchipinda chamkati* nʼkuyeza chipilala chamʼmbali chapakhomo ndipo anapeza kuti kuchindikala kwake chinali mikono iwiri. Anapezanso kuti khomo linali mikono 6 ndipo makoma a khomolo anali* mikono 7.
3 Kenako analowa mʼchipinda chamkati* nʼkuyeza chipilala chamʼmbali chapakhomo ndipo anapeza kuti kuchindikala kwake chinali mikono iwiri. Anapezanso kuti khomo linali mikono 6 ndipo makoma a khomolo anali* mikono 7.