-
Ezekieli 41:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Mʼmbali zonse za kachisiyo munali masitepe oyenda chozungulira opitira mʼzipinda zamʼmwamba amene ankakulirakulira akamakwera mʼmwamba.+ Zipinda za nsanjika yachitatu zinali zokulirapo kuposa za nsanjika yachiwiri, ndipo zipinda za nsanjika yachiwiri zinali zokulirapo kuposa za nyumba yapansi. Munthu akafuna kupita kuzipinda zamʼmwamba kuchokera kuzipinda zapansi ankadutsa mʼzipinda zapakati.
-