Ezekieli 41:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Khoma lakunja la zipinda zamʼmbali linali lochindikala mikono 5. Panali mpata* kuchokera mʼmphepete mwa maziko kukafika pamene panayambira khoma la zipinda zamʼmbali zimene zinali mbali ya kachisi.
9 Khoma lakunja la zipinda zamʼmbali linali lochindikala mikono 5. Panali mpata* kuchokera mʼmphepete mwa maziko kukafika pamene panayambira khoma la zipinda zamʼmbali zimene zinali mbali ya kachisi.