-
Ezekieli 41:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Pakati pa zipinda zamʼmbali ndi mpata umene unali mbali yakumpoto panali khomo ndipo khomo lina linali mbali yakumʼmwera. Mpatawo unali mikono 5 mulifupi, kuzungulira mbali zonse.
-