-
Ezekieli 41:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Kumadzulo kwa kachisi kunalinso nyumba ina imene inayangʼanizana ndi malo opanda kanthu. Nyumbayi inali mikono 70 mulifupi ndipo mulitali mwake inali mikono 90. Khoma la nyumbayo linali lochindikala mikono 5, kuzungulira nyumba yonseyo.
-