Ezekieli 41:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Nkhope ya munthu inayangʼana mtengo wa kanjedza kumbali imodzi ndipo nkhope ya mkango* inayangʼana mtengo wa kanjedza kumbali inayo.+ Zithunzizi zinajambulidwa mofanana kuzungulira kachisi yenseyo.
19 Nkhope ya munthu inayangʼana mtengo wa kanjedza kumbali imodzi ndipo nkhope ya mkango* inayangʼana mtengo wa kanjedza kumbali inayo.+ Zithunzizi zinajambulidwa mofanana kuzungulira kachisi yenseyo.